David Kuthyola

Matamando Lyrics

Matamando video

Votes:
0
Wrong lyrics?

David Kuthyola - Matamando lyrics

ndiimba matamando
popeza ndinu oyera
ndikhulupira inu
tate wa dziko lonse

chorus

wa zakumwamba ndi zapansi
ayenera matamandoDavid Kuthyola - Matamando - http://motolyrics.com/david-kuthyola/matamando-lyrics.html
ine ndikhulupila iye
tate wadziko lonse

ndiimba matamando
ndinu oyera mnjira zonse
inu mundiyang'anira
masiku amoyo wanga

back to chorus

Write a comment

What do you think about song "Matamando"? Let us know in the comments below!

Recommended songs