KBG

Zoononga Moyo Lyrics

Zoononga Moyo video

No photo
Overview
Votes:
0
Wrong lyrics?

KBG - Zoononga Moyo lyrics

Verse 1:LAWI
Amati bawa
ndi njira yochotsela nkhawa
nanga bwanji ukadzuka mmawa
matsile maluzi uliso confused
ndingonena chindunji
chenicheni nchiti
chokhalila mfiti
when in actual sense you r a slave to the sin that yo glue to
iwe tchimo litavala umunthu
chonde ndithandizeni
ndidziweko swaga as much as i know ndizoononga moyo wanga
sikuzikweza kodi?
Kuwalila kodi?
Kukhutitsidwa ndimmene ndavalila kodi?
Inde asungwana apapa mukukhwana titha kuyamikila mpakana kupanga mwana
KBG - Zoononga Moyo - http://motolyrics.com/kbg/zoononga-moyo-lyrics.html
Inde abwana mwatchena osanama but check on the . . . Ndiyesu mwasemphana
u can be who u want to b
multiply zinthu ngati tyms
u can buy evrything with paper
but heaven uuuh uuuh zachisoni pepa

{Chorus:}
kodi wapindulanji iweyo
utapeza zonse zofuna mtima wako
koma zonse zomwe wapezazo
mulibe chipulumutso
ndizinthu zoonona moyo wako x2

Verse2:KBG
lawi nane ndiwauze fanzi
. . . .

Write a comment

What do you think about song "Zoononga Moyo"? Let us know in the comments below!

Recommended songs