- Votes:
- See also:
Revolver - Sindidanda Remix lyrics
Intro(krazie g)
yezzir officialy served
this is the remix ladies and gentlmen
or ladies just ladies i dont mind
anyway uhmm revolver you know what it is
the daredevilz,krazie g,gwambizzle and that hypa man
lets get hyper then,yezzir lets go
verse 1(krazie g)
yezzir krazie g is tha name yo
i cant fight koma beats ndimamenya
akazi kundikakamila ngati k pa kenya
kuwafunsila amachotsa k'yo ndikuti enya
kudanda sindinkatha nde n'nakupanga abandon
fanzi ikufuna ndidande ine makani ngati ada amboni
and giving a f**k has never been an option
even if i wanted babies i would go with adoption
enanu mu rap game muno takudabwam'moni
mukamba bwanji za beef mukudya abwan'noni
nde mukamandibeefa ,muziziwa ndinu aphwete ka
sindiyankha,ndimangoseka mpaka m'mimba kupweteka
nigga am tha shit,ask the suer tanks,men
am on fire you can ask llyod banks
this shit is too easy i did it with ma mouth closed
its krazie g and i see you with my eyes closed
chorus(GD)
akafuna kuthoka ine
sindidanda
busy pokopoko za ine
sindidanda
pamwamba sindichoka ine
sindidanda
ndine mfana wotopa ine
sindidanda
akati oooooooooh
sindidanda
akati oooooooooh
sindidanda
akati oooooooooh
sindidanda
verse 2(hypa)
terminator of the game komatu sine swazi
they be biting & feeding my rhymes nkona ali athanzi
if you drive mumatope doesnt mean you ridin dirty
tikuwonelani ngati muli maliseche
ndimatha kuimba olo opanda credit
am changing this game busy kuipanga edit
you wanna be my form kalembe std 8
zopusa sindipanga ndithu ngati ndine virgin
nkona sindidanda when they busy hating me
i punchline alot maybe i should try boxin
they criticise alot maybe they should try hating
do a track with me ukainvela ndi angelo
cause am killing every rapper pano ndili pa bello
calling me the best ndimangoyankha hello
read between the lines if you know how to phanda
hypa ndi shasha ma haters angodanda
Revolver - Sindidanda Remix - http://motolyrics.com/revolver/sindidanda-remix-lyrics.html
verse 3(gwamba)
ndikudziwika mu ghetto
ngati deni ya kwa bush d
round horse pa beat hip hop ine ndi bruce lee
fanzi kuthokathoka ine osadanda
kuyesesa kundiyabwa ine osakanda
ndine blank space fanzi imandifila
ndikumenya ma beat kuwasiya akulila
mwana iwe suli sick ukunama ukungoyatsemula
ndikudya sister wako nde usandiyese mula
nthawi yakwana ngati ndinacthela alarm
sober nje ukandifuna undipeza m'balamu
chi chi chifana chodzinva ngati chikuzithoka chokha
chili ill,ma rhymes chikungo vokha
ku church ndine B.A munyimbo ndine murderer
pa deni ndine last born munyimbo ndine fazala
ndine rap soldier koma ndili mu civilian
munva kuwawa simunati ingopililani
(back to hook)
verse 4 (Revolver)
i dont know what love is
but i got enough cheese
to make you drop my pants and suck these nuts
number 4 in the charts
first nigga rapping at a show when it starts
see i aint star yet,but am getting there
battle any mc if he can dare
we taking over makape mwakhalitsa
ama run this ngati man wa callista
but for now chimahopu chindigwanda
agwila tay ndikatchuka ndichilanda
ya'll know chidracula sichidanda
i drink alot koma nfana sindibanda
nde ndimasowa heavy ndikagwila
mwanakazi amanva kunowa chikanjira
chigoli,tikamaonela mpila
lelo ndakwanitsa 16 mwandilira
verse 5(Gd)
gd say wat say wat
kuchiitanila bawa sichigwanda
bawa pang'ono man chayamba kublander
ndicholimba simungachiteme ndichi ganda
dollar ikavuta kidnap david banda
mwaona ndayambe kale kupalamula
kamwa yaikulu ngati mvuu kuyatsamula
ndidzatenga injunction yahwe akamadzagamula
kumwaza dola ngati chipani cholamula
its a remix if you didnt know what this is
i aint gat nutn to prove am not a thesis
ya'll cats is full of shit because you stinkin of feaces
ama get high defying the laws of physicz(iwe)
killer on loose am about to make a killin
always been a hero now am about to be a villan
niggas and bitches get your hands up to tha ceilin
m-dub chillin Lo-budget in the building
back to hook(*2)