National Anthem

Malawi Native Anthem Text Lyrics

Malawi Native Anthem Text video

Votes:
0
See also:
Wrong lyrics?

National Anthem - Malawi Native Anthem Text lyrics

1.
Mlungu dalitsani Malawi,
Mumsunge m'mtendere.
Gonjetsani adani onse,
Njala, nthenda, nsanje.
Lunzitsani mitima yathu,
Kuti tisaope.
Mdalitse Mtsogo leri na fe,
Ndi Mai Malawi.
2.
Malawi ndziko lokongola,
La chonde ndi ufulu,
Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri,
Ndithudi tadala.National Anthem - Malawi Native Anthem Text - http://motolyrics.com/national-anthem/malawi-native-anthem-text-lyrics.html
Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,
N'mphatso zaulere.
Nkhalango, madambo abwino.
Ngwokoma Malawi.
3.
O! Ufulu tigwirizane,
Kukweza Malawi.
Ndi chikondi, khama, kumvera,
Timutumikire.
Pa nkhondo nkana pa mtendere,
Cholinga n'chimodzi.
Mai, bambo, tidzipereke,
Pokweza Malawi.
Sent by Carlos André Pereira da Silva Branco

Write a comment

What do you think about song "Malawi Native Anthem Text"? Let us know in the comments below!

More "Other Songs A - SAI" Album Lyrics

Recommended songs